-
Luka 17:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 “Ndani wa inu angauze kapolo wake amene wangofika kumene kuchokera ku ntchito yolima kapena yoweta nkhosa kuti, ‘Fika kutebulo kuno msanga udzadye’?
-