-
Luka 19:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Yesu atafika pamalopo, anayang’ana m’mwambamo n’kumuuza kuti: “Zakeyu, fulumira tsika, chifukwa lero ndiyenera kukakhala m’nyumba mwako.”
-