-
Luka 21:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Koma zinthu izi zikadzayamba kuchitika, mudzaimirire chilili ndi kutukula mitu yanu, chifukwa chipulumutso chanu chikuyandikira.”
-