Luka 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kumwamba ndi dziko lapansi zidzachoka,+ koma mawu anga sadzachoka ayi.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:33 Kukambitsirana, ptsa. 133-134 Nsanja ya Olonda,6/1/1988, tsa. 30