Luka 21:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Masana Yesu anali kuphunzitsa m’kachisi,+ koma usiku anali kupita kukagona kuphiri lotchedwa phiri la Maolivi.+
37 Masana Yesu anali kuphunzitsa m’kachisi,+ koma usiku anali kupita kukagona kuphiri lotchedwa phiri la Maolivi.+