Yohane 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Panaonekera munthu wina amene anatumidwa monga nthumwi ya Mulungu.+ Dzina lake anali Yohane.+