Yohane 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Yohane anachitiranso umboni kuti: “Ndinaona mzimu ukutsika ngati nkhunda kuchokera kumwamba, ndipo unakhalabe pa iye.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:32 Nsanja ya Olonda,12/1/2007, tsa. 26
32 Yohane anachitiranso umboni kuti: “Ndinaona mzimu ukutsika ngati nkhunda kuchokera kumwamba, ndipo unakhalabe pa iye.+