Yohane 1:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Koma Natanayeli anamufunsa kuti: “Kodi mu Nazareti mungatuluke kanthu kabwino?”+ Pamenepo Filipo anati: “Tiye ukaone.” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:46 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2021, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,8/15/2002, tsa. 13
46 Koma Natanayeli anamufunsa kuti: “Kodi mu Nazareti mungatuluke kanthu kabwino?”+ Pamenepo Filipo anati: “Tiye ukaone.”