Yohane 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi inu ndinu wamkulu+ kuposa kholo lathu Yakobo, amene anatipatsa chitsimechi, chimenenso iyeyo, ana ake ndi ng’ombe zake anali kumwa?” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:12 “Wotsatira Wanga,” tsa. 77
12 Kodi inu ndinu wamkulu+ kuposa kholo lathu Yakobo, amene anatipatsa chitsimechi, chimenenso iyeyo, ana ake ndi ng’ombe zake anali kumwa?”