-
Yohane 5:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kenako Yesu anapeza munthu uja m’kachisi ndi kumuuza kuti: “Onatu wachira tsopano. Usakachimwenso, kuti chinachake choopsa kuposa matenda chisadzakuchitikire.”
-