Yohane 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yesu ananena kuti: “Akhazikeni pansi anthuwa muja amakhalira pa chakudya.”+ Pamalopo panali udzu wambiri. Choncho amuna pafupifupi 5,000 anakhaladi pansi.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:10 Yesu—Ndi Njira, tsa. 128 Nsanja ya Olonda,9/1/1987, ptsa. 16-17
10 Yesu ananena kuti: “Akhazikeni pansi anthuwa muja amakhalira pa chakudya.”+ Pamalopo panali udzu wambiri. Choncho amuna pafupifupi 5,000 anakhaladi pansi.+