Yohane 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano anthuwo ataona zizindikiro zimene anachitazo, anayamba kunena kuti: “Mosakayika uyu ndi mneneri+ uja amene anati adzabwera padziko.” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:14 Nsanja ya Olonda,7/1/2010, tsa. 22
14 Tsopano anthuwo ataona zizindikiro zimene anachitazo, anayamba kunena kuti: “Mosakayika uyu ndi mneneri+ uja amene anati adzabwera padziko.”