-
Yohane 6:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Tsiku lotsatira, anthu amene anaima kutsidya lina la nyanjayo anaona kuti ngalawa ina palibe koma pali imodzi yokha yaing’ono. Choncho anadziwa kuti Yesu sanakwere ngalawa pamodzi ndi ophunzira ake koma kuti ophunzira akewo anachoka paokha.
-