Yohane 6:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Ine ndine chakudya chopatsa moyo. Aliyense wobwera kwa ine sadzamva njala ngakhale pang’ono, ndipo wokhulupirira mwa ine sadzamva ludzu.+
35 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Ine ndine chakudya chopatsa moyo. Aliyense wobwera kwa ine sadzamva njala ngakhale pang’ono, ndipo wokhulupirira mwa ine sadzamva ludzu.+