Yohane 6:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Sikuti alipo munthu amene anaonapo Atate ayi,+ kupatulapo yekhayo amene anachokera kwa Mulungu, ameneyu anaona Atate.+
46 Sikuti alipo munthu amene anaonapo Atate ayi,+ kupatulapo yekhayo amene anachokera kwa Mulungu, ameneyu anaona Atate.+