-
Yohane 6:52Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
52 Pamenepo Ayudawo anayamba kutsutsana okhaokha, kuti: “Kodi munthu uyu angathe bwanji kutipatsa mnofu wake kuti tidye?”
-