Yohane 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero abale ake+ anamupempha kuti: “Mupite ku Yudeya kuti ophunzira anunso akaone zimene mukuchita. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:3 Yesu—Ndi Njira, tsa. 154 Nsanja ya Olonda,3/15/1988, tsa. 24
3 Chotero abale ake+ anamupempha kuti: “Mupite ku Yudeya kuti ophunzira anunso akaone zimene mukuchita.