Yohane 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo panali manong’onong’o ambiri onena za iye m’khamu lonse la anthulo.+ Ena anali kunena kuti: “Amene uja ndi munthu wabwino.” Ndipo ena anali kunena kuti: “Ayi si munthu wabwino amene uja, iye akusocheretsa anthu ambiri.”
12 Ndipo panali manong’onong’o ambiri onena za iye m’khamu lonse la anthulo.+ Ena anali kunena kuti: “Amene uja ndi munthu wabwino.” Ndipo ena anali kunena kuti: “Ayi si munthu wabwino amene uja, iye akusocheretsa anthu ambiri.”