Yohane 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Lekani kuweruza poona maonekedwe akunja, koma muziweruza ndi chiweruzo cholungama.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:24 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2018, ptsa. 8-12 Nsanja ya Olonda,11/1/1989, ptsa. 28-30