Yohane 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pamenepa anali kunena za mzimu umene onse okhulupirira mwa iye anali pafupi kulandira. Pakuti pa nthawiyi n’kuti asanaulandire,+ chifukwa Yesu anali asanalandire ulemerero wake.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:39 Nsanja ya Olonda,4/15/1988, tsa. 8
39 Pamenepa anali kunena za mzimu umene onse okhulupirira mwa iye anali pafupi kulandira. Pakuti pa nthawiyi n’kuti asanaulandire,+ chifukwa Yesu anali asanalandire ulemerero wake.+