-
Yohane 7:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Tsopano alonda aja anabwerera kwa ansembe aakulu ndi Afarisi. Ndiyeno iwowa anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani simunabwere naye?”
-