Yohane 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ananena mawu amenewa ali m’malo a zopereka+ pamene anali kuphunzitsa m’kachisi. Koma palibe amene anamugwira,+ chifukwa nthawi yake+ inali isanafikebe.
20 Ananena mawu amenewa ali m’malo a zopereka+ pamene anali kuphunzitsa m’kachisi. Koma palibe amene anamugwira,+ chifukwa nthawi yake+ inali isanafikebe.