Yohane 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndili ndi zambiri zoti ndinene zokhudza inu ndi kuperekerapo chiweruzo. Ndipotu amene anandituma ine amanena zoona. Zimene ndinamva kwa iye, zomwezo ndikuzilankhula m’dzikoli.”+
26 Ndili ndi zambiri zoti ndinene zokhudza inu ndi kuperekerapo chiweruzo. Ndipotu amene anandituma ine amanena zoona. Zimene ndinamva kwa iye, zomwezo ndikuzilankhula m’dzikoli.”+