Yohane 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndipo amene ananditumayo ali ndi ine. Iye sandisiya ndekha, chifukwa ndimachita zinthu zomukondweretsa nthawi zonse.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:29 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16
29 Ndipo amene ananditumayo ali ndi ine. Iye sandisiya ndekha, chifukwa ndimachita zinthu zomukondweretsa nthawi zonse.”+