Yohane 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yesu atamva zimenezi ananena kuti: “Kudwala kumeneku si kwa imfa chabe, koma n’kopatsa Mulungu ulemerero,+ kuti mwa kudwalako, Mwana wa Mulungu alemekezeke.” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:4 Nsanja ya Olonda,9/15/2013, tsa. 329/15/2000, ptsa. 14-15
4 Koma Yesu atamva zimenezi ananena kuti: “Kudwala kumeneku si kwa imfa chabe, koma n’kopatsa Mulungu ulemerero,+ kuti mwa kudwalako, Mwana wa Mulungu alemekezeke.”