Yohane 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopano Mariya atafika kumene kunali Yesu kuja ndi kumuona, anagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi pafupi ndi mapazi a Yesu. Kenako anamuuza kuti: “Ambuye, mukanakhala kuno mlongo wanga sakanamwalira.”+
32 Tsopano Mariya atafika kumene kunali Yesu kuja ndi kumuona, anagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi pafupi ndi mapazi a Yesu. Kenako anamuuza kuti: “Ambuye, mukanakhala kuno mlongo wanga sakanamwalira.”+