Yohane 11:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Yesu anati: “Chotsani chimwalachi.”+ Marita, mlongo wa womwalirayo anauza Yesu kuti: “Ambuye, pano ayenera kuti wayamba kununkha, pakuti lero ndi tsiku lachinayi chimuikireni m’manda.” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:39 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 30
39 Yesu anati: “Chotsani chimwalachi.”+ Marita, mlongo wa womwalirayo anauza Yesu kuti: “Ambuye, pano ayenera kuti wayamba kununkha, pakuti lero ndi tsiku lachinayi chimuikireni m’manda.”