Yohane 11:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Tsopano pasika+ wa Ayuda anali pafupi, ndipo anthu ochuluka anachoka m’midzi ndi kupita ku Yerusalemu pasikayo asanafike, kuti akachite mwambo wa kudziyeretsa.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:55 Yesu—Ndi Njira, tsa. 236 Nsanja ya Olonda,10/15/1989, tsa. 86/1/1989, tsa. 8
55 Tsopano pasika+ wa Ayuda anali pafupi, ndipo anthu ochuluka anachoka m’midzi ndi kupita ku Yerusalemu pasikayo asanafike, kuti akachite mwambo wa kudziyeretsa.+