Yohane 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano anthu ambiri amene analipo pamene iye anaitana Lazaro+ kuti atuluke m’manda achikumbutso ndi kumuukitsa, anali kumuchitira umboni.+
17 Tsopano anthu ambiri amene analipo pamene iye anaitana Lazaro+ kuti atuluke m’manda achikumbutso ndi kumuukitsa, anali kumuchitira umboni.+