Yohane 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tomasi+ anafunsa kuti: “Ambuye, ife sitikudziwa kumene mukupita.+ Ndiye njira yake tingaidziwe bwanji?” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:5 Yesu—Ndi Njira, tsa. 274 Nsanja ya Olonda,8/1/1990, tsa. 8
5 Tomasi+ anafunsa kuti: “Ambuye, ife sitikudziwa kumene mukupita.+ Ndiye njira yake tingaidziwe bwanji?”