Yohane 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu mukanandidziwa ine, mukanadziwanso Atate wanga. Kuyambira panopa mwawadziwa ndipo mwawaona.”+