Yohane 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndikanapanda kuchita pakati pawo ntchito zimene wina aliyense sanachitepo,+ akanakhala opanda tchimo,+ koma tsopano aona ndipo adana nane, ndi kudananso ndi Atate wanga.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:24 Yesu—Ndi Njira, tsa. 277 Nsanja ya Olonda,8/15/1990, tsa. 9
24 Ndikanapanda kuchita pakati pawo ntchito zimene wina aliyense sanachitepo,+ akanakhala opanda tchimo,+ koma tsopano aona ndipo adana nane, ndi kudananso ndi Atate wanga.+