Yohane 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pa tsiku limenelo+ simudzandifunsanso mafunso. Ndithudi ndikukuuzani, Ngati mupempha chilichonse+ kwa Atate m’dzina langa adzakupatsani.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:23 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 1 2021 tsa. 10 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 17
23 Pa tsiku limenelo+ simudzandifunsanso mafunso. Ndithudi ndikukuuzani, Ngati mupempha chilichonse+ kwa Atate m’dzina langa adzakupatsani.+