Yohane 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo m’chimake.+ Kodi sindiyenera kumwa za m’kapu imene Atate wandipatsa,+ zivute zitani?” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:11 Yesu—Ndi Njira, tsa. 284 Nsanja ya Olonda,9/1/2002, tsa. 1010/15/1990, ptsa. 8-9
11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo m’chimake.+ Kodi sindiyenera kumwa za m’kapu imene Atate wandipatsa,+ zivute zitani?”