Yohane 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akapolo ndi alonda anali ataima chapomwepo, pakuti anali atakoleza moto wamakala,+ chifukwa kunali kuzizira ndipo anali kuwotha motowo. Nayenso Petulo anaimirira pamodzi ndi iwo n’kumawotha nawo. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:18 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
18 Akapolo ndi alonda anali ataima chapomwepo, pakuti anali atakoleza moto wamakala,+ chifukwa kunali kuzizira ndipo anali kuwotha motowo. Nayenso Petulo anaimirira pamodzi ndi iwo n’kumawotha nawo.