Machitidwe 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu ameneyu, monga woperekedwa mwa kufuna kwa Mulungu ndi kudziwiratu kwake zam’tsogolo,+ ndi amene inu munamukhomerera pamtengo ndi kumupha kudzera mwa anthu osamvera malamulo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:23 Galamukani!,8/8/1993, ptsa. 12-13 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 12
23 Munthu ameneyu, monga woperekedwa mwa kufuna kwa Mulungu ndi kudziwiratu kwake zam’tsogolo,+ ndi amene inu munamukhomerera pamtengo ndi kumupha kudzera mwa anthu osamvera malamulo.+