Machitidwe 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iye anali mneneri, ndipo anali kudziwa kuti Mulungu anam’lonjeza mwa lumbiro, kuti pampando wake wachifumu adzakhazikapo mmodzi mwa zipatso za m’chiuno mwake.+
30 Iye anali mneneri, ndipo anali kudziwa kuti Mulungu anam’lonjeza mwa lumbiro, kuti pampando wake wachifumu adzakhazikapo mmodzi mwa zipatso za m’chiuno mwake.+