Machitidwe 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 kuti: “Tichite nawo chiyani amuna amenewa?+ Chifukwa kunena zoona, iwo achitadi chizindikiro chachikulu, chimene chaonekera kwa onse okhala mu Yerusalemu.+ Ndipo ife sitingatsutse zimenezi.
16 kuti: “Tichite nawo chiyani amuna amenewa?+ Chifukwa kunena zoona, iwo achitadi chizindikiro chachikulu, chimene chaonekera kwa onse okhala mu Yerusalemu.+ Ndipo ife sitingatsutse zimenezi.