Machitidwe 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo anyamata anabwera ndi kumukulunga pansalu.+ Kenako anatuluka naye ndi kukamuika m’manda.