-
Machitidwe 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Petulo anamufunsa kuti: “Tandiuza, kodi ndalama zonse zimene awirinu mwapeza mutagulitsa munda wanu ndi izi?” Iye anayankha kuti: “Inde, ndi zomwezo.”
-