Machitidwe 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Mulungu ananenanso kuti mbewu yake idzakhala alendo+ m’dziko lachilendo,+ ndipo anthu adzawasandutsa akapolo ndi kuwasautsa kwa zaka 400.+
6 Ndipo Mulungu ananenanso kuti mbewu yake idzakhala alendo+ m’dziko lachilendo,+ ndipo anthu adzawasandutsa akapolo ndi kuwasautsa kwa zaka 400.+