-
Machitidwe 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Makamu a anthu anali kutchera khutu ndi mtima umodzi ndi kumvetsera zimene Filipo anali kunena. Iwo anali kumvetsera ndi kuona zizindikiro zimene iye anali kuchita.
-