Machitidwe 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumeneko kunali anthu ambiri ogwidwa ndi mizimu yonyansa,+ ndipo inali kufuula mokweza mawu ndi kutuluka. Ndipo anthu ambiri amene anali akufa ziwalo+ ndi olumala anali kuchiritsidwa.
7 Kumeneko kunali anthu ambiri ogwidwa ndi mizimu yonyansa,+ ndipo inali kufuula mokweza mawu ndi kutuluka. Ndipo anthu ambiri amene anali akufa ziwalo+ ndi olumala anali kuchiritsidwa.