Machitidwe 8:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho atatha kuchitira umboni mokwanira ndi kulankhula mawu a Yehova, anabwerera ku Yerusalemu. Pamene anali kubwerera anali kulengeza uthenga wabwino m’midzi yambiri ya Asamariya.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:25 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54
25 Choncho atatha kuchitira umboni mokwanira ndi kulankhula mawu a Yehova, anabwerera ku Yerusalemu. Pamene anali kubwerera anali kulengeza uthenga wabwino m’midzi yambiri ya Asamariya.+