Machitidwe 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anati: “Mbuyanga, ndinu ndani kodi?” Anamuyankha kuti: “Ndine Yesu, amene iwe ukumuzunza.+