Machitidwe 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nthawi yomweyo anayamba kulalikira za Yesu m’masunagoge,+ kuti Ameneyu ndiye Mwana wa Mulungu. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:20 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 63-64