Machitidwe 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho usiku, ophunzira ake anamuika m’dengu ndi kumutulutsira pawindo la mpanda, n’kumutsitsira kunja.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:25 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 64 Nsanja ya Olonda,1/15/2005, tsa. 296/1/1990, tsa. 18
25 Choncho usiku, ophunzira ake anamuika m’dengu ndi kumutulutsira pawindo la mpanda, n’kumutsitsira kunja.+