Machitidwe 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamenepo mpingo+ mu Yudeya monse, mu Galileya, ndi mu Samariya unalowa m’nyengo yamtendere, ndipo unakhala wolimba. Popeza kuti unali kuyenda moopa Yehova+ ndiponso kulimbikitsidwa ndi mzimu woyera,+ mpingowo unali kukulirakulira. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:31 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 65-66 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2017, tsa. 13 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 314/15/2007, tsa. 226/1/1990, tsa. 15
31 Pamenepo mpingo+ mu Yudeya monse, mu Galileya, ndi mu Samariya unalowa m’nyengo yamtendere, ndipo unakhala wolimba. Popeza kuti unali kuyenda moopa Yehova+ ndiponso kulimbikitsidwa ndi mzimu woyera,+ mpingowo unali kukulirakulira.
9:31 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 65-66 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2017, tsa. 13 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 314/15/2007, tsa. 226/1/1990, tsa. 15