Machitidwe 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Tsopano Petulo anamupatsa dzanja lake ndi kumuimiritsa.+ Atatero anaitana oyerawo ndi akazi amasiye aja, ndipo anamupereka kwa iwo ali wamoyo.+
41 Tsopano Petulo anamupatsa dzanja lake ndi kumuimiritsa.+ Atatero anaitana oyerawo ndi akazi amasiye aja, ndipo anamupereka kwa iwo ali wamoyo.+