Machitidwe 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iyeyu anali wopembedza+ ndi woopa+ Mulungu pamodzi ndi banja lake lonse. Anali kupatsa anthu mphatso zambiri zachifundo+ ndipo anali kupemphera kwa Mulungu nthawi zonse.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:2 Nsanja ya Olonda,1/15/1990, tsa. 6
2 Iyeyu anali wopembedza+ ndi woopa+ Mulungu pamodzi ndi banja lake lonse. Anali kupatsa anthu mphatso zambiri zachifundo+ ndipo anali kupemphera kwa Mulungu nthawi zonse.+